Mateyu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana.+ Maliko 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana ndiponso kudzakhala njala.+ Zimenezi ndi chiyambi cha mavuto aakulu.*+
7 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana.+
8 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana ndiponso kudzakhala njala.+ Zimenezi ndi chiyambi cha mavuto aakulu.*+