Maliko 14:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu mʼkachisi nʼkumaphunzitsa,+ koma simunandigwire. Komabe, izi zikuchitika kuti Malemba akwaniritsidwe.”+
49 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu mʼkachisi nʼkumaphunzitsa,+ koma simunandigwire. Komabe, izi zikuchitika kuti Malemba akwaniritsidwe.”+