Luka 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anapita naye ku Yerusalemu ndipo anamukweza pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi* nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, mudziponye pansi kuchokera pano.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2016, tsa. 323/2016, ptsa. 31-32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 36
9 Kenako anapita naye ku Yerusalemu ndipo anamukweza pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi* nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, mudziponye pansi kuchokera pano.+