Luka 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Eliya sanatumizidwe kwa aliyense wa akazi amenewo. Mʼmalomwake anatumizidwa kwa mkazi wamasiye ku Zarefati mʼdziko la Sidoni.+
26 Koma Eliya sanatumizidwe kwa aliyense wa akazi amenewo. Mʼmalomwake anatumizidwa kwa mkazi wamasiye ku Zarefati mʼdziko la Sidoni.+