Luka 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Eliya sanatumizidwe kwa aliyense wa akazi amenewo. M’malomwake anatumizidwa kwa mkazi wamasiye ku Zarefati+ m’dziko la Sidoni.
26 Koma Eliya sanatumizidwe kwa aliyense wa akazi amenewo. M’malomwake anatumizidwa kwa mkazi wamasiye ku Zarefati+ m’dziko la Sidoni.