1 Mafumu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Eliya ananyamuka kupita ku Zarefati n’kulowa pachipata cha mzindawo. Kenako anaona mayi, mkazi wamasiye, akutola nkhuni. Ndiyeno anamuitana n’kumuuza kuti: “Undipatseko madzi pang’ono m’chikho kuti ndimwe.”+
10 Chotero Eliya ananyamuka kupita ku Zarefati n’kulowa pachipata cha mzindawo. Kenako anaona mayi, mkazi wamasiye, akutola nkhuni. Ndiyeno anamuitana n’kumuuza kuti: “Undipatseko madzi pang’ono m’chikho kuti ndimwe.”+