Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Nthawi yomweyo mtumiki wa Abulahamuyo anamuthamangira n’kumuuza kuti: “Chonde ndipatse madzi a mumtsuko wako ndimweko pang’ono.”+

  • Mateyu 10:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha m’kapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pang’ono.”+

  • Yohane 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno mayi wina wa mu Samariya anafika kudzatunga madzi. Yesu anapempha mayiyo kuti: “Mundipatseko madzi akumwa mayi.”

  • Aheberi 11:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa,+ anachekedwa pakati ndi macheka, anaphedwa+ mwankhanza ndi lupanga, anayendayenda atavala zikopa za nkhosa+ ndi zikopa za mbuzi pamene anali osowa,+ pamene anali m’masautso+ komanso pamene anali kuzunzidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena