Aheberi 11:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa, anadulidwa pakati, anaphedwa ndi lupanga+ ndiponso anayendayenda atavala zikopa za nkhosa ndi zikopa za mbuzi.+ Ankasowa zinthu, ankazunzidwa+ komanso ankakumana ndi mavuto ena.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:37 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, ptsa. 18-19
37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa, anadulidwa pakati, anaphedwa ndi lupanga+ ndiponso anayendayenda atavala zikopa za nkhosa ndi zikopa za mbuzi.+ Ankasowa zinthu, ankazunzidwa+ komanso ankakumana ndi mavuto ena.+