Luka 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sangalalani pa tsiku limenelo ndipo mudumphedumphe mokondwera, chifukwa mphoto imene Mulungu adzakupatseni ndi yaikulu,* popeza zinthu zimenezo ndi zimenenso makolo awo akale anachitira aneneri.+
23 Sangalalani pa tsiku limenelo ndipo mudumphedumphe mokondwera, chifukwa mphoto imene Mulungu adzakupatseni ndi yaikulu,* popeza zinthu zimenezo ndi zimenenso makolo awo akale anachitira aneneri.+