Luka 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kondwerani pa tsiku limenelo ndi kudumphadumpha, chifukwa mphoto yanu ndi yaikulu kumwamba, pakuti zomwezo ndi zimenenso makolo awo akale anachitira aneneri.+
23 Kondwerani pa tsiku limenelo ndi kudumphadumpha, chifukwa mphoto yanu ndi yaikulu kumwamba, pakuti zomwezo ndi zimenenso makolo awo akale anachitira aneneri.+