Luka 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi mukamakonda anthu okhawo amene amakukondani, mudzapindula chiyani? Chifukwa ngakhale ochimwa amakonda anthu okhawo amene amawakonda.+
32 Kodi mukamakonda anthu okhawo amene amakukondani, mudzapindula chiyani? Chifukwa ngakhale ochimwa amakonda anthu okhawo amene amawakonda.+