Luka 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso, siyani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Siyani kutsutsa ena ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:37 Yandikirani, ptsa. 162-164 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 910/1/1990, tsa. 22
37 Komanso, siyani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Siyani kutsutsa ena ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+