Luka 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kenako anawauzanso fanizo lakuti: “Munthu wosaona sangatsogolere wosaona mnzake, angatero ngati? Ngati angatero onse awiri angagwere mʼdzenje, si choncho?+
39 Kenako anawauzanso fanizo lakuti: “Munthu wosaona sangatsogolere wosaona mnzake, angatero ngati? Ngati angatero onse awiri angagwere mʼdzenje, si choncho?+