Luka 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kenako anawauzanso fanizo lakuti: “Wakhungu sangatsogolere wakhungu mnzake, angatero ngati? Ngati atatero onse awiri angagwere m’dzenje, si choncho kodi?+
39 Kenako anawauzanso fanizo lakuti: “Wakhungu sangatsogolere wakhungu mnzake, angatero ngati? Ngati atatero onse awiri angagwere m’dzenje, si choncho kodi?+