Luka 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pasanapite nthawi yaitali, Yesu anayamba kuyenda mumzinda ndi mzinda komanso mudzi ndi mudzi nʼkumalalikira komanso kulengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu.+ Ndipo atumwi 12 aja anali naye limodzi. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16
8 Pasanapite nthawi yaitali, Yesu anayamba kuyenda mumzinda ndi mzinda komanso mudzi ndi mudzi nʼkumalalikira komanso kulengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu.+ Ndipo atumwi 12 aja anali naye limodzi.