Luka 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Jowana+ mkazi wa Kuza amene anali kapitawo wa Herode, Suzana ndi azimayi ena ambiri, amene ankatumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,8/15/2015, ptsa. 29-306/1/2003, ptsa. 4-5
3 Jowana+ mkazi wa Kuza amene anali kapitawo wa Herode, Suzana ndi azimayi ena ambiri, amene ankatumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo.+