Luka 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Jowana+ mkazi wa Kuza kapitawo wa Herode, Suzana ndi amayi ena ambiri, amene anali kutumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,8/15/2015, ptsa. 29-306/1/2003, ptsa. 4-5
3 Jowana+ mkazi wa Kuza kapitawo wa Herode, Suzana ndi amayi ena ambiri, amene anali kutumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo.