Luka 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno gulu lalikulu la anthu litasonkhana, limodzi ndi ena amene ankamulondola kuchokera mʼmizinda yosiyanasiyana, Yesu anafotokoza fanizo lakuti:+
4 Ndiyeno gulu lalikulu la anthu litasonkhana, limodzi ndi ena amene ankamulondola kuchokera mʼmizinda yosiyanasiyana, Yesu anafotokoza fanizo lakuti:+