Luka 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno khamu lalikulu la anthu litasonkhana, limodzi ndi ena amene anali kumulondola kuchokera m’mizinda yosiyanasiyana, Yesu anawafotokozera fanizo kuti:+
4 Ndiyeno khamu lalikulu la anthu litasonkhana, limodzi ndi ena amene anali kumulondola kuchokera m’mizinda yosiyanasiyana, Yesu anawafotokozera fanizo kuti:+