Luka 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu atangotsika nʼkufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina wogwidwa ndi chiwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo ankangokhala wosavala, komanso sankakhala mʼnyumba, koma kumanda.*+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 114 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 65/15/1987, tsa. 26
27 Yesu atangotsika nʼkufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina wogwidwa ndi chiwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo ankangokhala wosavala, komanso sankakhala mʼnyumba, koma kumanda.*+