Luka 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma atangotsika n’kufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina waziwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo anali kungokhala osavala, komanso sanali kukhala kunyumba, koma kumanda.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 114 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 65/15/1987, tsa. 26
27 Koma atangotsika n’kufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina waziwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo anali kungokhala osavala, komanso sanali kukhala kunyumba, koma kumanda.+