-
Luka 8:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 (Chifukwa Yesu ankauza mzimu wonyansawo kuti utuluke mwa munthuyo. Mzimu umenewu unamugwira mwamphamvu maulendo ambiri.*+ Mobwerezabwereza ankamumanga ndi maunyolo komanso matangadza nʼkumamuyangʼanira. Koma chifukwa cha mphamvu ya chiwandacho, ankadula maunyolowo nʼkuthawira kumalo opanda anthu.)
-