-
Luka 8:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 (Pakuti iye anali kuuza mzimu wonyansawo kuti utuluke mwa munthuyo. Mzimu umenewu unamugwira mwamphamvu+ kwa nthawi yaitali ndithu. Mobwerezabwereza anali kumumanga ndi maunyolo komanso matangadza n’kumamuyang’anira. Koma chifukwa cha mphamvu ya chiwandacho, anali kudula maunyolowo ndi kuthawira kumalo opanda anthu.)
-