Luka 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno gulu lalikulu la nkhumba+ linkadya paphiri kumeneko. Choncho ziwandazo zinamuchonderera kuti azilole kukalowa munkhumbazo ndipo iye anazilola.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:32 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, ptsa. 26-27
32 Ndiyeno gulu lalikulu la nkhumba+ linkadya paphiri kumeneko. Choncho ziwandazo zinamuchonderera kuti azilole kukalowa munkhumbazo ndipo iye anazilola.+