Luka 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano gulu lalikulu ndithu la nkhumba+ linali kudya paphiri kumeneko. Chotero ziwandazo zinamuchonderera kuti azilole kukalowa munkhumbazo.+ Ndipo iye anazilola. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:32 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, ptsa. 26-27
32 Tsopano gulu lalikulu ndithu la nkhumba+ linali kudya paphiri kumeneko. Chotero ziwandazo zinamuchonderera kuti azilole kukalowa munkhumbazo.+ Ndipo iye anazilola.