Luka 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Herode,* wolamulira chigawo,* anamva zonse zimene zinkachitika. Iye anathedwa nzeru chifukwa ena ankanena kuti Yohane waukitsidwa.+
7 Tsopano Herode,* wolamulira chigawo,* anamva zonse zimene zinkachitika. Iye anathedwa nzeru chifukwa ena ankanena kuti Yohane waukitsidwa.+