Luka 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo anawafunsa kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu wa Mulungu.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:20 Tsanzirani, ptsa. 190-191 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 26
20 Pamenepo anawafunsa kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu wa Mulungu.”+