-
Luka 9:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Mzimu umamugwira, ndipo mwadzidzidzi amafuula, kenako umamuchititsa kuti aphuphe kwinaku akuchita thovu. Mzimu umenewu umamuvulaza kwambiri ndipo zimavuta kuti umusiye.
-