Luka 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mzimu umam’gwira, ndipo mwadzidzidzi amafuula, kenako umam’tsalimitsa kwinaku akuchita thovu. Mzimu+ umenewu umamuvulaza kwambiri ndipo suchoka msanga.
39 Mzimu umam’gwira, ndipo mwadzidzidzi amafuula, kenako umam’tsalimitsa kwinaku akuchita thovu. Mzimu+ umenewu umamuvulaza kwambiri ndipo suchoka msanga.