Luka 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Yesu ndi ophunzira akewo ali kwaokha, anawauza kuti: “Osangalala ndi anthu amene akuona zimene inu mukuonazi.+
23 Ndiyeno Yesu ndi ophunzira akewo ali kwaokha, anawauza kuti: “Osangalala ndi anthu amene akuona zimene inu mukuonazi.+