-
Luka 10:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Poyankha Yesu ananena kuti: “Munthu wina ankayenda kuchokera ku Yerusalemu kupita ku Yeriko ndipo anakumana ndi achifwamba amene anamuvula nʼkumumenya koopsa. Kenako anachoka, nʼkumusiya atatsala pangʼono kufa.
-