-
Luka 10:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Poyankha Yesu anati: “Munthu wina anali kuyenda kuchokera ku Yerusalemu kupita ku Yeriko. Ndipo anakumana ndi achifwamba amene anam’vula ndi kumumenya koopsa. Kenako anapita, n’kumusiya ali pafupi kufa.
-