-
Luka 11:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsopano Yesu ankapemphera pamalo enaake. Atamaliza, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Ambuye, tiphunzitseni kupemphera ngati mmene Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.”
-