Luka 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anali kupemphera pamalo enaake. Atatsiriza, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Ambuye, tiphunzitseni kupemphera,+ ngati mmene Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 174 Nsanja ya Olonda,2/1/2004, tsa. 87/15/1996, tsa. 35/15/1990, tsa. 158/1/1988, ptsa. 8-9
11 Tsopano Yesu anali kupemphera pamalo enaake. Atatsiriza, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Ambuye, tiphunzitseni kupemphera,+ ngati mmene Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.”+
11:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 174 Nsanja ya Olonda,2/1/2004, tsa. 87/15/1996, tsa. 35/15/1990, tsa. 158/1/1988, ptsa. 8-9