Luka 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuuza kuti: “Ophunzira a Yohane amasala kudya kawirikawiri ndi kupemphera mopembedzera. Ophunzira a Afarisi amachitanso chimodzimodzi, koma anuwa amangodya ndi kumwa.”+
33 Iwo anamuuza kuti: “Ophunzira a Yohane amasala kudya kawirikawiri ndi kupemphera mopembedzera. Ophunzira a Afarisi amachitanso chimodzimodzi, koma anuwa amangodya ndi kumwa.”+