18 Ophunzira a Yohane ndi Afarisi anali kusala kudya. Choncho iwo anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ophunzira a Yohane ndi ophunzira a Afarisi amasala kudya, koma ophunzira anu sasala kudya?”+
34 Kunabwera Mwana wa munthu ndipo iye akudya ndi kumwa, koma inu mumati, ‘Taonani! Munthu wosusuka ndi wokonda kwambiri vinyo, bwenzi la okhometsa msonkho ndi ochimwa!’+