Mateyu 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako ophunzira a Yohane anabwera kwa iye n’kumufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ife ndi Afarisi timasala kudya koma ophunzira anu sasala kudya?”+ Luka 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuuza kuti: “Ophunzira a Yohane amasala kudya kawirikawiri ndi kupemphera mopembedzera. Ophunzira a Afarisi amachitanso chimodzimodzi, koma anuwa amangodya ndi kumwa.”+
14 Kenako ophunzira a Yohane anabwera kwa iye n’kumufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ife ndi Afarisi timasala kudya koma ophunzira anu sasala kudya?”+
33 Iwo anamuuza kuti: “Ophunzira a Yohane amasala kudya kawirikawiri ndi kupemphera mopembedzera. Ophunzira a Afarisi amachitanso chimodzimodzi, koma anuwa amangodya ndi kumwa.”+