Luka 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa mʼmalo opanda madzi kufunafuna malo okhala, koma akapanda kupezeka, umanena kuti, ‘Ndibwerera kunyumba yanga imene ndinatulukamo ija.’+
24 Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa mʼmalo opanda madzi kufunafuna malo okhala, koma akapanda kupezeka, umanena kuti, ‘Ndibwerera kunyumba yanga imene ndinatulukamo ija.’+