Luka 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa m’malo ouma kufunafuna malo okhala, koma akapanda kupezeka, umanena kuti, ‘Ndibwerera m’nyumba yanga mmene ndinatuluka muja.’+
24 “Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa m’malo ouma kufunafuna malo okhala, koma akapanda kupezeka, umanena kuti, ‘Ndibwerera m’nyumba yanga mmene ndinatuluka muja.’+