Luka 11:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho Ambuye anamuuza kuti: “Inu Afarisi muli ngati kapu ndi mbale zimene zatsukidwa kunja kokha koma mkati mwake muli mwakuda. Mkati mwa mitima yanu mwadzaza dyera ndi zinthu zoipa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:39 Yesu—Ndi Njira, tsa. 178 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 24
39 Choncho Ambuye anamuuza kuti: “Inu Afarisi muli ngati kapu ndi mbale zimene zatsukidwa kunja kokha koma mkati mwake muli mwakuda. Mkati mwa mitima yanu mwadzaza dyera ndi zinthu zoipa.+