Luka 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho ngati inu simungathe kuchita zimenezi, nʼchifukwa chiyani mukuda nkhawa ndi zinthu zinazo?+
26 Choncho ngati inu simungathe kuchita zimenezi, nʼchifukwa chiyani mukuda nkhawa ndi zinthu zinazo?+