Luka 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atamva zimenezi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wosangalala ndi munthu amene adzadye chakudya* mu Ufumu wa Mulungu.” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:15 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 8
15 Atamva zimenezi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wosangalala ndi munthu amene adzadye chakudya* mu Ufumu wa Mulungu.”