Luka 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atamva izi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wodala ndi munthu wakudya chakudya mu ufumu wa Mulungu.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:15 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 8
15 Atamva izi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wodala ndi munthu wakudya chakudya mu ufumu wa Mulungu.”+