-
Luka 17:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Pa tsiku limenelo, munthu amene adzakhale padenga la nyumba koma katundu wake ali mʼnyumba, asadzatsike kukatenga katundu wakeyo. Chimodzimodzinso munthu amene adzakhale ali mʼmunda, asadzabwerere ku zinthu zimene wazisiya mʼmbuyo.
-