-
Luka 17:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 “Pa tsiku limenelo, munthu amene adzakhale padenga la nyumba koma katundu wake ali m’nyumbamo, asadzatsike kukatenga katundu wakeyo. Chimodzimodzinso munthu amene adzakhale ali m’munda, asadzabwerere ku zinthu zimene wazisiya m’mbuyo.
-