Luka 19:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Afarisi ena mʼgululo anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, adzudzuleni ophunzira anuwa.”+