Luka 19:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Afarisi ena m’khamulo anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, adzudzuleni ophunzira anuwa.”+