Luka 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi ina, pamene anthu ena ankalankhula za kachisi, mmene anamukongoletsera ndi miyala yabwino kwambiri komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu,+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 255 Nsanja ya Olonda,3/1/1990, tsa. 25
5 Nthawi ina, pamene anthu ena ankalankhula za kachisi, mmene anamukongoletsera ndi miyala yabwino kwambiri komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu,+