Luka 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso, mukadzamva phokoso la nkhondo ndi zipolowe,* musadzachite mantha. Chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika choyamba, koma mapeto sadzafika nthawi yomweyo.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:9 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32
9 Komanso, mukadzamva phokoso la nkhondo ndi zipolowe,* musadzachite mantha. Chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika choyamba, koma mapeto sadzafika nthawi yomweyo.”+