-
Luka 22:60Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
60 Koma Petulo anati: “Munthu iwe, ine sindikudziwa zimene ukunena.” Nthawi yomweyo mawu ali mʼkamwa, tambala analira.
-